2 Samueli 23:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo mau otsiriza a Davide ndi awa: Atero Davide mwana wa Yese, atero munthu wokwezedwa, ndiye wodzozedwa wa Mulungu wa Yakobo, ndi mwini nyimbo yokoma ya Israele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo mau otsiriza a Davide ndi awa, Atero Davide mwana wa Yese, atero munthu wokwezedwa, ndiye wodzozedwa wa Mulungu wa Yakobo, ndi mwini nyimbo yokoma ya Israele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Naŵa mau otsiriza a Davide: Nayi nyimbo ya Davide, mwana wa Yese, mau a munthu amene Mulungu adamkweza pamwamba, amene Mulungu wa Yakobe adamdzoza kuti akhale mfumu, munthu wokonda kuimba nyimbo zokoma za Israele: Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Nawa mawu otsiriza a Davide: “Mawu a Davide mwana wa Yese, mawu a munthu amene wakwezedwa ndi Wammwambamwamba, munthu wodzozedwa ndi Mulungu wa Yakobo, woyimba nyimbo za Israeli: Onani mutuwo |