2 Samueli 23:2 - Buku Lopatulika2 Mzimu wa Yehova unalankhula mwa ine, ndi mau ake anali pa lilime langa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Mzimu wa Yehova unalankhula mwa ine, ndi mau ake anali pa lilime langa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 “Mzimu wa Chauta ukulankhula mwa ine, mau ake ali pakamwa panga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 “Mzimu wa Yehova unayankhula kudzera mwa ine; mawu ake anali pakamwa panga. Onani mutuwo |