Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Samueli 23:2 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 “Mzimu wa Yehova unayankhula kudzera mwa ine; mawu ake anali pakamwa panga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

2 Mzimu wa Yehova unalankhula mwa ine, ndi mau ake anali pa lilime langa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Mzimu wa Yehova unalankhula mwa ine, ndi mau ake anali pa lilime langa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 “Mzimu wa Chauta ukulankhula mwa ine, mau ake ali pakamwa panga.

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 23:2
6 Mawu Ofanana  

Mbuye wanga mfumu, maso a Aisraeli onse ali pa inu, kuti adziwe kuchokera kwa inu amene adzakhala pa mpando waufumu wa mbuye wanga mʼmalo mwanu.


Iye anawawuza kuti, “Nanga zikutheka bwanji kuti Davide poyankhula mwa Mzimu Woyera amatchula Iye ‘Ambuye?’ Pakuti akuti,


Pajatu Davide mwini wake, poyankhula mwa Mzimu Woyera, ananena kuti, “Ambuye anati kwa Ambuye anga: ‘Khalani pa dzanja langa lamanja kufikira nditayika adani anu pansi pa mapazi anu.’


Pakuti mawu a uneneri sanadze mwa kufuna kwa anthu, koma anthu anayankhula zochokera kwa Mulungu, Mzimu Woyera atawayankhulitsa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa