Mateyu 22:43 - Buku Lopatulika43 Iye anati kwa iwo, Ndipo Davide mu Mzimu amtchula Iye bwanji Ambuye, nanena, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201443 Iye anati kwa iwo, Ndipo Davide mu Mzimu amtchula Iye bwanji Ambuye, nanena, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa43 Iye adaŵafunsa kuti, “Tsono bwanji nanga Davideyo ndi nzeru zochokera kwa Mzimu Woyera, akutchula Mpulumutsi wolonjezedwa uja kuti Mbuye wake? Paja adati, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero43 Iye anawawuza kuti, “Nanga zikutheka bwanji kuti Davide poyankhula mwa Mzimu Woyera amatchula Iye ‘Ambuye?’ Pakuti akuti, Onani mutuwo |