Mateyu 22:42 - Buku Lopatulika42 nati, Muganiza bwanji za Khristu? Ali mwana wa yani? Iwo ananena kwa Iye, Wa Davide. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201442 nati, Muganiza bwanji za Khristu? Ali mwana wa yani? Iwo ananena kwa Iye, Wa Davide. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa42 Adati, “Mumaganiza chiyani za Mpulumutsi wolonjezedwa uja? Mumati ndi mwana wa yani?” Iwo aja adati, “Ndi mwana wa Davide.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero42 “Kodi mukuganiza bwanji za Khristu? Ndi Mwana wa ndani?” Iwo anayankha kuti, “Mwana wa Davide.” Onani mutuwo |