2 Samueli 1:25 - Buku Lopatulika Ha! Amphamvuwo anagwa pakati pa nkhondo! Yonatani anaphedwa pamisanje pako. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ha! Amphamvuwo anagwa pakati pa nkhondo! Yonatani anaphedwa pamisanje pako. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa “Ha! Kani amphamvu agwa motere! Yonatani ali gone, atafa pa zitunda zako zachipembedzo. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero “Taonani amphamvu agwa ku nkhondo! Yonatani wagona ataphedwa ku zitunda. |
Ana aakazi inu a Israele, mulirire Saulo, amene anakuvekani ndi zofiira zokometsetsa, amene anaika zokometsetsa zagolide pa zovala zanu.