2 Samueli 1:24 - Buku Lopatulika24 Ana aakazi inu a Israele, mulirire Saulo, amene anakuvekani ndi zofiira zokometsetsa, amene anaika zokometsetsa zagolide pa zovala zanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Ana akazi inu a Israele, mulirire Saulo, amene anakuvekani ndi zofiira zokometsetsa, amene anaika zokometsetsa zagolide pa zovala zanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 “Inu akazi a ku Israele, mlireni Saulo. Chifukwa cha iye uja munkavala zovala zabwino zofiira, ndiponso munkaika zokometsera zagolide pa zovala zanu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 “Inu ana aakazi a Israeli, mulireni Sauli, amene anakuvekani zovala zofiira ndi zofewa, amene anakometsera zovala zanu ndi zokometsera zagolide. Onani mutuwo |