2 Samueli 1:25 - Buku Lopatulika25 Ha! Amphamvuwo anagwa pakati pa nkhondo! Yonatani anaphedwa pamisanje pako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Ha! Amphamvuwo anagwa pakati pa nkhondo! Yonatani anaphedwa pamisanje pako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 “Ha! Kani amphamvu agwa motere! Yonatani ali gone, atafa pa zitunda zako zachipembedzo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 “Taonani amphamvu agwa ku nkhondo! Yonatani wagona ataphedwa ku zitunda. Onani mutuwo |