Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Samueli 1:25 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

25 “Taonani amphamvu agwa ku nkhondo! Yonatani wagona ataphedwa ku zitunda.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

25 Ha! Amphamvuwo anagwa pakati pa nkhondo! Yonatani anaphedwa pamisanje pako.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

25 Ha! Amphamvuwo anagwa pakati pa nkhondo! Yonatani anaphedwa pamisanje pako.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

25 “Ha! Kani amphamvu agwa motere! Yonatani ali gone, atafa pa zitunda zako zachipembedzo.

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 1:25
6 Mawu Ofanana  

“Ulemerero wako iwe Israeli, wagona utaphedwa ku zitunda. Taonani amphamvu agwa kumeneko!


“Inu ana aakazi a Israeli, mulireni Sauli, amene anakuvekani zovala zofiira ndi zofewa, amene anakometsera zovala zanu ndi zokometsera zagolide.


“Taonani amphamvu agwa! Zida zankhondo zawonongeka!”


Chipewa chathu chaufumu chagwa pamutu pathu. Tsoka kwa ife, chifukwa tachimwa!


Azebuloni ndi anthu amene anayika moyo wawo mʼzoopsa. Nawonso anthu a fuko la Nafutali anayika miyoyo yawo pa chiswe pomenya nkhondo pamwamba pa mapiri.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa