Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Samueli 1:27 - Buku Lopatulika

27 Ha! Amphamvuwo anagwa, ndi zida za nkhondo zinaonongeka.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

27 Ha! Amphamvuwo anagwa, ndi zida za nkhondo zinaonengeka.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

27 “Ha! Kani amphamvu agwa motere, zida zao zankhondo nkuwonongeka!”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

27 “Taonani amphamvu agwa! Zida zankhondo zawonongeka!”

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 1:27
7 Mawu Ofanana  

Ulemerero wako, Israele, unaphedwa pa misanje yako. Ha! Adagwa amphamvu!


Ha! Amphamvuwo anagwa pakati pa nkhondo! Yonatani anaphedwa pamisanje pako.


Ndipo Elisa anadwala nthenda ija adafa nayo, namtsikira Yehowasi mfumu ya Israele, namlirira, nati, Atate wanga, atate wanga, galeta wa Israele ndi apakavalo ake!


Ndipo Elisa anapenya, nafuula, Atate wanga, atate wanga, galeta wa Israele ndi apakavalo ake! Koma analibe kumpenyanso; nagwira zovala zakezake, nazing'amba pakati.


Aletsa nkhondo ku malekezero a dziko lapansi; athyola uta, nadula nthungo; atentha magaleta ndi moto.


Achokera m'dziko lakutali, kumalekezero a thambo, ngakhale Yehova, ndi zida za mkwiyo wake, kuti aononge dziko lonse.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa