1 Samueli 15:4 - Buku Lopatulika Ndipo Saulo anamemeza anthu, nawawerenga ku Telaimu, akuyenda pansi zikwi mazana awiri, ndi a kwa Yuda anthu zikwi khumi. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Saulo anamemeza anthu, nawawerenga ku Telaimu, akuyenda pansi zikwi mazana awiri, ndi a kwa Yuda anthu zikwi khumi. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Choncho Saulo adaitana ankhondo ake, naŵaŵerenga ku Telaimu. Ankhondo oyenda pansi analipo 200,000, ankhondo a ku Yuda analipo 10,000 pamodzi. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Kotero Sauli anayitana ankhondo ake nawawerenga ku Telaimu. Ankhondo oyenda pansi analipo 200,000 ndipo mwa iwowa 10,000 anali a fuko la Yuda. |
Ndipo anawawerenga ku Bezeki; ndipo ana a Israele anali zikwi mazana atatu, ndi anthu a Yuda ndiwo zikwi makumi atatu.
Ndipo Samuele anauka nachoka ku Giligala kunka ku Gibea wa ku Benjamini. Ndipo Saulo anawerenga anthu amene anali naye, monga mazana asanu ndi limodzi.