1 Samueli 11:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo anawawerenga ku Bezeki; ndipo ana a Israele anali zikwi mazana atatu, ndi anthu a Yuda ndiwo zikwi makumi atatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo anawawerenga ku Bezeki; ndipo ana a Israele anali zikwi mazana atatu, ndi anthu a Yuda ndiwo zikwi makumi atatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Saulo adaŵasonkhanitsa ku Bezeki, naŵaŵerenga. Aisraele analipo 300,000, Ayuda analipo 30,000. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Pamenepo Sauli anawasonkhanitsa ku Bezeki nawawerenga, ndipo Aisraeli analipo 300,000, Ayuda analipo 30,000. Onani mutuwo |