1 Samueli 13:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo Samuele anauka nachoka ku Giligala kunka ku Gibea wa ku Benjamini. Ndipo Saulo anawerenga anthu amene anali naye, monga mazana asanu ndi limodzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo Samuele anauka nachoka ku Giligala kunka ku Gibea wa ku Benjamini. Ndipo Saulo anawerenga anthu amene anali naye, monga mazana asanu ndi limodzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Atatero Samuele adanyamuka ku Giligala napita ku Gibea ku dziko la Benjamini. Saulo adaŵerenga anthu amene anali naye, ndipo adapeza kuti alipo 600. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Kenaka Samueli anachoka ku Giligala ndi kupita ku Gibeyati ku dziko la Benjamini. Saulo anawerenga anthu amene anali naye ndipo analipo 600. Onani mutuwo |