Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Samueli 15:5 - Buku Lopatulika

5 Ndipo Saulo anafika kumzinda wa Amaleke, nalalira kuchigwa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Ndipo Saulo anafika kumudzi wa Amaleke, nalalira kuchigwa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Ndipo Saulo adafika ku mzinda wa Aamaleke, naubisalira m'khwaŵa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Sauli anapita ku mzinda wa Aamaleki nawubisalira mʼkhwawa.

Onani mutuwo Koperani




1 Samueli 15:5
4 Mawu Ofanana  

Ndipo anatenga amuna ngati zikwi zisanu, nawaika m'molalira pakati pa Betele ndi Ai, kumadzulo kwa mzinda.


nawalamulira ndi kuti, Taonani, muzikhala olalira kukhonde kwa mzinda; musakhalira kutali ndi mzinda, koma mukhale okonzekeratu nonse;


Ndipo Saulo anamemeza anthu, nawawerenga ku Telaimu, akuyenda pansi zikwi mazana awiri, ndi a kwa Yuda anthu zikwi khumi.


Ndipo Saulo anauza Akeni kuti, Mukani, chokani mutsike kutuluka pakati pa Aamaleke, kuti ndingakuonongeni pamodzi ndi iwo; pakuti inu munachitira ana a Israele onse zabwino, pakufuma iwo ku Ejipito. Chomwecho Akeni anachoka pakati pa Aamaleke.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa