1 Samueli 15:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo Saulo anamemeza anthu, nawawerenga ku Telaimu, akuyenda pansi zikwi mazana awiri, ndi a kwa Yuda anthu zikwi khumi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo Saulo anamemeza anthu, nawawerenga ku Telaimu, akuyenda pansi zikwi mazana awiri, ndi a kwa Yuda anthu zikwi khumi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Choncho Saulo adaitana ankhondo ake, naŵaŵerenga ku Telaimu. Ankhondo oyenda pansi analipo 200,000, ankhondo a ku Yuda analipo 10,000 pamodzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Kotero Sauli anayitana ankhondo ake nawawerenga ku Telaimu. Ankhondo oyenda pansi analipo 200,000 ndipo mwa iwowa 10,000 anali a fuko la Yuda. Onani mutuwo |