1 Samueli 15:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo Saulo anauza Akeni kuti, Mukani, chokani mutsike kutuluka pakati pa Aamaleke, kuti ndingakuonongeni pamodzi ndi iwo; pakuti inu munachitira ana a Israele onse zabwino, pakufuma iwo ku Ejipito. Chomwecho Akeni anachoka pakati pa Aamaleke. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo Saulo anauza Akeni kuti, Mukani, chokani mutsike kutuluka pakati pa Aamaleke, kuti ndingakuonongeni pamodzi ndi iwo; pakuti inu munachitira ana a Israele onse zabwino, pakufuma iwo ku Ejipito. Chomwecho Akeni anachoka pakati pa Aamaleke. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Tsono adauza Akeni kuti, “Muchoke pakati pa Aamaleke, kuti ndingakuwonongereni kumodzi. Pakuti inu mudachitira chifundo Aisraele muja ankachokera ku Ejipitomu.” Motero Akeni adachoka pakati pa Aamaleke. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Tsono Sauli anawuza Akeni kuti, “Samukani, muchoke pakati pa Aamaleki kuti ine ndisakuwonongeni pamodzi ndi iwo pakuti inu munaonetsa kukoma mtima kwa Aisraeli onse pamene ankatuluka mʼdziko la Igupto,” Choncho Akeni anachoka pakati pa Aamaleki. Onani mutuwo |