Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 10:3 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Pamene akuliza malipenga onse awiri, anthu onse asonkhane kwa iwe pa khomo la tenti ya msonkhano.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

3 Akaliza, khamu lonse lisonkhane kuli iwe ku khomo la chihema chokomanako.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Akaliza, khamu lonse lisonkhane kuli iwe ku khomo la chihema chokomanako.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Akaliza aŵiri onsewo, mpingo wonse usonkhane kwa iwe pa chipata cha chihema chamsonkhano.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 10:3
3 Mawu Ofanana  

“Lengeza ku Yuda ndi kulalikira mu Yerusalemu kuti, ‘Lizani lipenga mʼdziko lonse!’ Ndipo fuwulani kuti, ‘Sonkhanani! Tiyeni tithawire ku mizinda yotetezedwa!’


Lizani lipenga mu Ziyoni. Chenjezani pa phiri langa loyera. Onse okhala mʼdziko anjenjemere, pakuti tsiku la Yehova likubwera, layandikira;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa