Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 10:4 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Akaliza limodzi lokha, atsogoleri, akulu a mafuko a Aisraeli, asonkhane kwa iwe.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

4 Akaliza limodzi, pamenepo akalonga, akulu a zikwi a mu Israele, azisonkhana kuli iwe.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Akaliza limodzi, pamenepo akalonga, akulu a zikwi a m'Israele, azisonkhana kuli iwe.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Koma akangoliza limodzi lokha, atsogoleri a mafuko a Aisraele ndiwo asonkhane kwa iwe.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 10:4
4 Mawu Ofanana  

Koma sankhani amuna odziwa ntchito yawo, anthu owopa Mulungu, anthu odalirika amene amadana ndi kupeza phindu mwachinyengo. Tsono muwayike kuti akhale oyangʼanira anthu motere: atsogoleri a anthu 1,000, ena a anthu 100, ena a anthu 50 ndi ena a anthu khumi.


Kenaka atsogoleri a Aisraeli, akuluakulu a mabanja omwe ankayangʼanira mafuko a anthu omwe anawawerenga aja, anachita chopereka.


Choncho ndinatenga anthu otsogolera mafuko anu, anzeru ndi omwe mumawalemekeza, ndipo ndinawayika kuti azikulamulirani mʼmagulu a 1,000, ena 100, ena makumi asanu ndi ena khumi, kuti akhalenso ngati akapitawo a mafuko.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa