Numeri 10:3 - Buku Lopatulika3 Akaliza, khamu lonse lisonkhane kuli iwe ku khomo la chihema chokomanako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Akaliza, khamu lonse lisonkhane kuli iwe ku khomo la chihema chokomanako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Akaliza aŵiri onsewo, mpingo wonse usonkhane kwa iwe pa chipata cha chihema chamsonkhano. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Pamene akuliza malipenga onse awiri, anthu onse asonkhane kwa iwe pa khomo la tenti ya msonkhano. Onani mutuwo |