Numeri 10:4 - Buku Lopatulika4 Akaliza limodzi, pamenepo akalonga, akulu a zikwi a mu Israele, azisonkhana kuli iwe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Akaliza limodzi, pamenepo akalonga, akulu a zikwi a m'Israele, azisonkhana kuli iwe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Koma akangoliza limodzi lokha, atsogoleri a mafuko a Aisraele ndiwo asonkhane kwa iwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Akaliza limodzi lokha, atsogoleri, akulu a mafuko a Aisraeli, asonkhane kwa iwe. Onani mutuwo |