Numeri 10:5 - Buku Lopatulika5 Mukaliza chokweza ayende a m'zigono za kum'mawa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Mukaliza chokweza ayende a m'zigono za kum'mawa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Mukaliza lipenga lochenjeza, anthu a m'mahema akuvuma ayambepo ulendo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Akaliza lipenga lochenjeza, misasa yomwe ili kummawa iyambe kusamuka. Onani mutuwo |