Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 10:5 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Akaliza lipenga lochenjeza, misasa yomwe ili kummawa iyambe kusamuka.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

5 Mukaliza chokweza ayende a m'zigono za kum'mawa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Mukaliza chokweza ayende a m'zigono za kum'mawa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Mukaliza lipenga lochenjeza, anthu a m'mahema akuvuma ayambepo ulendo.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 10:5
5 Mawu Ofanana  

“Fuwula kwambiri, usaleke. Mawu ako amveke ngati lipenga. Uwawuze anthu anga za kulakwa kwawo; uwuze nyumba ya Yakobo za machimo awo.


Lizani lipenga mu Ziyoni. Chenjezani pa phiri langa loyera. Onse okhala mʼdziko anjenjemere, pakuti tsiku la Yehova likubwera, layandikira;


Magulu a msasa wa Yuda ndiwo anayamba kunyamuka potsata mbendera yawo. Mtsogoleri wa gulu lawo anali Naasoni mwana wa Aminadabu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa