Numeri 10:6 - Buku Lopatulika6 Mukalizanso chokweza, a m'zigono za kumwera ayende; alize chokweza pakumuka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Mukalizanso chokweza, a m'zigono za kumwera ayende; alize chokweza pakumuka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Mukaliza lipenga lochenjeza kachiŵiri, anthu a m'mahema akumwera ayambepo ulendo. Muziŵalizira lipenga lochenjezalo nthaŵi zonse akamanyamuka ulendo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Akaliza lipenga lochenjeza lachiwiri, misasa yakummwera iyambe kusamuka. Kuliza kwa lipenga lochenjeza kudzakhala chizindikiro choyamba ulendo. Onani mutuwo |