Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 10:6 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Akaliza lipenga lochenjeza lachiwiri, misasa yakummwera iyambe kusamuka. Kuliza kwa lipenga lochenjeza kudzakhala chizindikiro choyamba ulendo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

6 Mukalizanso chokweza, a m'zigono za kumwera ayende; alize chokweza pakumuka.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Mukalizanso chokweza, a m'zigono za kumwera ayende; alize chokweza pakumuka.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Mukaliza lipenga lochenjeza kachiŵiri, anthu a m'mahema akumwera ayambepo ulendo. Muziŵalizira lipenga lochenjezalo nthaŵi zonse akamanyamuka ulendo.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 10:6
3 Mawu Ofanana  

Kenaka magulu a msasa wa fuko la Rubeni ananyamuka potsatira mbendera yawo. Mtsogoleri wawo anali Elizuri mwana wa Sedeuri.


Pofuna kusonkhanitsa anthu, muziliza malipenga, koma mosiyana ndi mmene malipenga ochenjeza amalizidwira.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa