Numeri 10:7 - Buku Lopatulika7 Pomemeza msonkhano mulize, wosati chokweza ai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Pomemeza msonkhano mulize, wosati chokweza ai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Pamene mpingo wonse uyenera kusonkhana pamodzi, mulize lipenga, koma musalize lipenga lochenjeza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Pofuna kusonkhanitsa anthu, muziliza malipenga, koma mosiyana ndi mmene malipenga ochenjeza amalizidwira. Onani mutuwo |