Numeri 10:8 - Buku Lopatulika8 Ana aamuna a Aroni, ansembe, ndiwo aziliza malipenga; ndipo akhale kwa inu lemba losatha ku mibadwo yanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ana amuna a Aroni, ansembe, ndiwo aziliza malipenga; ndipo akhale kwa inu lemba losatha ku mibadwo yanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Ana a Aroni, ansembe aja, ndiwo aziliza malipenga. Ntchito ya malipengayi ndi lamulo lamuyaya pa mibadwo yanu yonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 “Ana a Aaroni, ansembe aja, ndiwo aziliza malipengawo. Zimenezi zikhale zokhazikika kwa inu ndi ku mibado yanu yonse. Onani mutuwo |