Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 10:7 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Pofuna kusonkhanitsa anthu, muziliza malipenga, koma mosiyana ndi mmene malipenga ochenjeza amalizidwira.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

7 Pomemeza msonkhano mulize, wosati chokweza ai.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Pomemeza msonkhano mulize, wosati chokweza ai.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Pamene mpingo wonse uyenera kusonkhana pamodzi, mulize lipenga, koma musalize lipenga lochenjeza.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 10:7
3 Mawu Ofanana  

Lizani lipenga mu Ziyoni. Chenjezani pa phiri langa loyera. Onse okhala mʼdziko anjenjemere, pakuti tsiku la Yehova likubwera, layandikira;


“Ana a Aaroni, ansembe aja, ndiwo aziliza malipengawo. Zimenezi zikhale zokhazikika kwa inu ndi ku mibado yanu yonse.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa