Zekariya 5:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo ndinati kwa mthenga wakulankhula ndi ine, Amenewa amuka naye kuti efayo? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo ndinati kwa mthenga wakulankhula ndi ine, Amenewa amuka naye kuti efayo? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Tsono ndidafunsa mngelo amene ankalankhula nane kuti, “Nanganso gondololi akupita nalo kuti?” Iye adandiyankha kuti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Ine ndinafunsa mngelo amene amayankhula nane kuti, “Dengulo akupita nalo kuti?” Onani mutuwo |