Yona 2:3 - Buku Lopatulika3 Pakuti munandiponya mwakuya m'kati mwa nyanja, ndipo madzi anandizinga; mafunde anu onse a nyondonyondo anandimiza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Pakuti munandiponya mwakuya m'kati mwa nyanja, ndipo madzi anandizinga; mafunde anu onse a nyondonyondo anandimiza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Mudandiponya m'nyanja yozama, m'kati mwenimweni mwa njanja, ndipo mweza wam'nyanjamo udandizungulira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Munandiponya mʼnyanja yozama, mʼkati mwenimweni mwa nyanja, ndipo madzi oyenda anandizungulira; mafunde anu onse ndi mkokomo wake zinandimiza. Onani mutuwo |