Numeri 9:16 - Buku Lopatulika16 Kudatero kosalekeza; mtambo umachiphimba, ndi moto umaoneka usiku. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Kudatero kosalekeza; mtambo umachiphimba, ndi moto umaoneka usiku. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Zinkachitika motero mosalekeza. Mtambowo unkaphimba chihema chamsonkhano masana, ndipo usiku unkaoneka ngati moto. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Zinkachitika motere mosalekeza: mtambo unkakhala pamwamba pa chihema, ndipo usiku unkaoneka ngati moto. Onani mutuwo |