Numeri 8:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo ubwere nao Alevi pakhomo pa chihema chokomanako; nuwasonkhanitse khamu lonse la ana a Israele; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo ubwere nao Alevi pakhomo pa chihema chokomanako; nuwasonkhanitse khamu lonse la ana a Israele; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Ubwere ndi Alevi pakhomo pa chihema chamsonkhano, ndipo usonkhanitse mpingo wonse wa Aisraele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Ubwere nawo Aleviwo kutsogolo kwa tenti ya msonkhano ndipo usonkhanitse gulu la Aisraeli. Onani mutuwo |