Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 8:10 - Buku Lopatulika

10 nubwere nao Alevi pamaso pa Yehova; ndi ana a Israele aike manja ao pa Alevi;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 nubwere nao Alevi pamaso pa Yehova; ndi ana a Israele aike manja ao pa Alevi;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Pamene ukuŵapereka Aleviwo pamaso pa Chauta, Aisraele asanjike manja ao pa Alevi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Ubwere nawo pamaso pa Yehova, ndipo Aisraeli asanjike manja awo pa iwo.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 8:10
7 Mawu Ofanana  

Ndipo aike dzanja lake pamutu pa nsembe yopsereza; ndipo idzalandiridwa m'malo mwake, imtetezere.


Ndipo akulu a khamulo aike manja ao pamutu pa ng'ombeyo, pamaso pa Yehova; naiphe ng'ombeyo pamaso pa Yehova.


Landira Alevi m'malo mwa oyamba kubadwa onse mwa ana a Israele, ndi ng'ombe za Alevi m'malo mwa ng'ombe zao; ndipo Alevi azikhala anga; Ine ndine Yehova.


amenewo anawaika pamaso pa atumwi; ndipo m'mene adapemphera, anaika manja pa iwo.


Usanyalapse mphatsoyo ili mwa iwe, yopatsidwa kwa iwe mwa chinenero, pamodzi ndi kuika kwa manja a akulu.


Usafulumira kuika manja pa munthu aliyense, kapena usayanjana nazo zoipa za eni; udzisunge wekha woyera mtima.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa