Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 8:9 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Ubwere nawo Aleviwo kutsogolo kwa tenti ya msonkhano ndipo usonkhanitse gulu la Aisraeli.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

9 Ndipo ubwere nao Alevi pakhomo pa chihema chokomanako; nuwasonkhanitse khamu lonse la ana a Israele;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Ndipo ubwere nao Alevi pakhomo pa chihema chokomanako; nuwasonkhanitse khamu lonse la ana a Israele;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Ubwere ndi Alevi pakhomo pa chihema chamsonkhano, ndipo usonkhanitse mpingo wonse wa Aisraele.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 8:9
4 Mawu Ofanana  

Ndipo anakhazikitsa ansembe ndi Alevi pa ntchito zawo zotumikira Mulungu mu Yerusalemu monga zinalembedwera mʼbuku la Mose.


“Ubwere ndi Aaroni ndi ana ake pa chipata cha tenti ya msonkhano ndipo uwasambitse ndi madzi.


ndipo usonkhanitse gulu la anthu pa khomo la tenti ya msonkhano.”


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa