Numeri 7:18 - Buku Lopatulika18 Tsiku lachiwiri Netanele mwana wa Zuwara, kalonga wa Isakara, anabwera nacho chake: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Tsiku lachiwiri Netanele mwana wa Zuwara, kalonga wa Isakara, anabwera nacho chake: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Netanele mwana wa Zuwara, mtsogoleri wa fuko la Isakara, adapereka zopereka zake pa tsiku lachiŵiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Pa tsiku lachiwiri, Natanieli mwana wa Zuwara, mtsogoleri wa Isakara, anabweretsa chopereka chake. Onani mutuwo |