Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 7:17 - Buku Lopatulika

17 ndi nsembe yoyamika, ng'ombe ziwiri, nkhosa zamphongo zisanu, atonde asanu, anaankhosa asanu a chaka chimodzi; ndicho chopereka cha Nasoni mwana wa Aminadabu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 ndi nsembe yoyamika, ng'ombe ziwiri, nkhosa zamphongo zisanu, atonde asanu, anaankhosa asanu a chaka chimodzi; ndicho chopereka cha Nasoni mwana wa Aminadabu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 Ndipo zoperekera nsembe yachiyanjano zinali izi: ng'ombe ziŵiri, nkhosa zamphongo zisanu, atonde asanu, ndi anaankhosa asanu amphongo a chaka chimodzi. Zimenezi ndizo zimene zinali zopereka za Nasoni mwana wa Aminadabu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 ndi ngʼombe zothena ziwiri, nkhosa zazimuna zisanu, mbuzi zazimuna zisanu ndi ana ankhosa asanu a chaka chimodzi kuti zikhale za nsembe yachiyanjano. Ichi chinali chopereka cha Naasoni mwana wa Aminadabu.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 7:17
5 Mawu Ofanana  

Tsiku lachiwiri Netanele mwana wa Zuwara, kalonga wa Isakara, anabwera nacho chake:


mwana wa Yese, mwana wa Obede, mwana wa Bowazi, mwana wa Salimoni, mwana wa Nasoni,


mwana wa Aminadabu, mwana wa Admini, mwana wa Arini, mwana wa Hezironi, mwana wa Perezi, mwana wa Yuda,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa