Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 7:16 - Buku Lopatulika

16 tonde mmodzi akhale nsembe yauchimo;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 tonde mmodzi akhale nsembe yauchimo;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Adaperekanso tonde mmodzi woperekera nsembe yopepesera machimo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 mbuzi yayimuna imodzi, nsembe ya machimo;

Onani mutuwo Koperani




Numeri 7:16
3 Mawu Ofanana  

akamdziwitsa kuchimwa kwake adachimwako, azidza nacho chopereka chake, ndicho tonde wopanda chilema;


Ndipo wansembe atengeko mwazi wa nsembe yauchimo ndi chala chake, nauike pa nyanga za guwa la nsembe yopsereza, ndi kuthira mwazi wake patsinde pa guwa la nsembe yopsereza.


ng'ombe yamphongo imodzi, nkhosa yamphongo imodzi, mwanawankhosa mmodzi wa chaka chimodzi, zikhale nsembe yopsereza;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa