Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 7:18 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 Pa tsiku lachiwiri, Natanieli mwana wa Zuwara, mtsogoleri wa Isakara, anabweretsa chopereka chake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

18 Tsiku lachiwiri Netanele mwana wa Zuwara, kalonga wa Isakara, anabwera nacho chake:

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 Tsiku lachiwiri Netanele mwana wa Zuwara, kalonga wa Isakara, anabwera nacho chake:

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 Netanele mwana wa Zuwara, mtsogoleri wa fuko la Isakara, adapereka zopereka zake pa tsiku lachiŵiri.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 7:18
4 Mawu Ofanana  

Netanieli mwana wa Zuwara, kuchokera ku fuko la Isakara,


Fuko la Isakara lidzamanga pafupi ndi Yuda. Mtsogoleri wa gulu la Isakara ndi Netanieli mwana wa Zuwara.


ndi ngʼombe zothena ziwiri, nkhosa zazimuna zisanu, mbuzi zazimuna zisanu ndi ana ankhosa asanu a chaka chimodzi kuti zikhale za nsembe yachiyanjano. Ichi chinali chopereka cha Naasoni mwana wa Aminadabu.


Chopereka chomwe anabwera nacho chinali mbale imodzi yasiliva yolemera kilogalamu imodzi, beseni limodzi lowazira lasiliva lolemera magalamu 800, molingana ndi muyeso wa ku malo opatulika. Mbale zonse zinali zodzaza ndi ufa wosalala wosakaniza ndi mafuta monga chopereka cha chakudya.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa