Numeri 7:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, Akalonga onse, yense pa tsiku lake, apereke zopereka zao za kupereka chiperekere guwa la nsembe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, Akalonga onse, yense pa tsiku lake, apereke zopereka zao za kupereka chiperekere guwa la nsembe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Apo Chauta adauza Mose kuti, “Atsogoleriwo azibwera ndi zopereka zao zopatulira guwa, mtsogoleri mmodzi pa tsiku.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Pakuti Yehova anawuza Mose kuti, “Tsiku lililonse mtsogoleri mmodzi azibweretsa chopereka chake chopatulira guwa lansembe.” Onani mutuwo |