Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 7:11 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Pakuti Yehova anawuza Mose kuti, “Tsiku lililonse mtsogoleri mmodzi azibweretsa chopereka chake chopatulira guwa lansembe.”

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

11 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, Akalonga onse, yense pa tsiku lake, apereke zopereka zao za kupereka chiperekere guwa la nsembe.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, Akalonga onse, yense pa tsiku lake, apereke zopereka zao za kupereka chiperekere guwa la nsembe.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Apo Chauta adauza Mose kuti, “Atsogoleriwo azibwera ndi zopereka zao zopatulira guwa, mtsogoleri mmodzi pa tsiku.”

Onani mutuwo Koperani




Numeri 7:11
5 Mawu Ofanana  

Guwa la nsembe litadzozedwa, atsogoleri anabweretsa zopereka zawo zopatulira guwa nazipereka paguwapo.


Amene anabweretsa chopereka chake tsiku loyamba anali Naasoni mwana wa Aminadabu wa fuko la Yuda.


Pakuti Mulungu si Mulungu wachisokonezo koma wamtendere. Monga mwa mipingo yonse ya oyera mtima.


Koma chilichonse chichitike moyenera ndi mwadongosolo.


Pakuti ngakhale sindili pakati panu mʼthupi, ndili nanu pamodzi mu mzimu, ndipo ndikukondwa kuona kuti mukulongosola bwino zonse ndiponso kuti chikhulupiriro chanu mwa Khristu ndi chokhazikika ndithu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa