Numeri 5:3 - Buku Lopatulika3 muwatulutse amuna ndi akazi muwatulutsire kunja kwa chigono, kuti angadetse chigono chao, chimene ndikhala m'kati mwakemo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 muwatulutse amuna ndi akazi muwatulutsire kunja kwa chigono, kuti angadetse chigono chao, chimene ndikhala m'kati mwakemo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Muchotse anthu onse otere, amuna kapena akazi. Muziŵatulutsira kunja kwa zithando kuti angaipitse zithando zao, poti Ine ndimakhala pakati pa anthu anga.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Muchotse amuna komanso amayi ndipo muwatulutsire kunja kwa msasa kuti asadetse msasa wawo kumene Ine ndimakhala pakati pawo.” Onani mutuwo |