Numeri 5:23 - Buku Lopatulika23 Ndipo wansembe alembere matemberero awa m'buku, ndi kuwafafaniza ndi madzi owawawa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndipo wansembe alembere matemberero awa m'buku, ndi kuwafafaniza ndi madzi owawawa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 “Wansembe alembe m'buku matemberero ameneŵa ndipo aŵafafanize poŵaviika m'madzi oŵaŵa aja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 “ ‘Wansembe alembe matemberero amenewa mʼbuku ndi kuwanyika mʼmadzi owawa aja. Onani mutuwo |