Numeri 5:24 - Buku Lopatulika24 Ndipo amwetse mkaziyo madzi owawa akudzetsa temberero; ndi madzi odzetsa temberero adzalowa mwa iye nadzamwawira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Ndipo amwetse mkaziyo madzi owawa akudzetsa temberero; ndi madzi odzetsa temberero adzalowa mwa iye nadzamwawira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Mkaziyo ayenera kumwa madzi oŵaŵawo, madzi amatemberero, mpaka aloŵe m'mimba mwake, kuti amve ululu woopsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Amwetse mkaziyo madzi owawawo omwe amabweretsa temberero, ndipo madzi amenewo adzalowa mʼmimba mwake ndi kuyambitsa ululu woopsa. Onani mutuwo |