Numeri 5:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo wansembe abwere naye, namuike pamaso pa Yehova; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo wansembe abwere naye, namuike pamaso pa Yehova; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 “Wansembe abwere ndi mkaziyo pafupi ndi kumuimika pamaso pa Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 “ ‘Wansembe abwere naye mkaziyo ndi kumuyimitsa pamaso pa Yehova. Onani mutuwo |