Numeri 5:17 - Buku Lopatulika17 natenge madzi opatulika m'mbale yadothi wansembeyo, natengeko fumbi lili pansi mu chihema, wansembeyo nalithire m'madzimo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 natenge madzi opatulika m'mbale yadothi wansembeyo, natengeko fumbi lili pansi m'Kachisi, wansembeyo nalithire m'madzimo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Wansembeyo atengeko madzi oyera m'mbiya, ndipo atapeko fumbi la m'Chihema cha Mulungu ndi kulithira m'madzimo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Ndipo wansembeyo atenge madzi oyera mʼmbiya ya dothi ndi kuyika mʼmadzimo fumbi lapansi la mʼTenti ya Msonkhano. Onani mutuwo |