Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 5:16 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 “ ‘Wansembe abwere naye mkaziyo ndi kumuyimitsa pamaso pa Yehova.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

16 Ndipo wansembe abwere naye, namuike pamaso pa Yehova;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Ndipo wansembe abwere naye, namuike pamaso pa Yehova;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 “Wansembe abwere ndi mkaziyo pafupi ndi kumuimika pamaso pa Chauta.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 5:16
6 Mawu Ofanana  

“Ine Yehova ndimafufuza mtima ndi kuyesa maganizo, ndimachitira munthu aliyense molingana ndi makhalidwe ake ndiponso moyenera ntchito zake.”


“ ‘Ngati munthu apereka nsembe yopsereza ya ngʼombe, ikhale yayimuna yopanda chilema. Aziyipereka pa khomo la tenti ya msonkhano, kuti Yehova alandire.


apite naye mkaziyo kwa wansembe. Ndipo popita atengenso gawo lakhumi la chopereka chaufa wa barele wokwana kilogalamu imodzi mʼmalo mwa mkaziyo. Asathire mafuta pa nsembeyo kapena lubani, chifukwa ndi nsembe ya chopereka ya chakudya yopereka chifukwa cha nsanje, nsembe yozindikiritsa tchimo.’ ”


Ndipo wansembeyo atenge madzi oyera mʼmbiya ya dothi ndi kuyika mʼmadzimo fumbi lapansi la mʼTenti ya Msonkhano.


Ukwati muziwulemekeza nonse, ndipo mwamuna ndi mkazi azikhala wokhulupirika, pakuti anthu adama ndi achigololo Mulungu adzawalanga.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa