Numeri 4:4 - Buku Lopatulika4 Ntchito ya ana a Kohati m'chihema chokomanako ndi iyi, kunena za zinthu zopatulika kwambiri: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ntchito ya ana a Kohati m'chihema chokomanako ndi iyi, kunena za zinthu zopatulika kwambiri: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Ntchito imene ana a Kohati ayenera kugwira m'chihema chamsonkhanomo ndi iyi: azisamala zinthu zopatulika kopambana. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 “Ntchito ya Akohati mu tenti ya msonkhano ndi iyi: kusamalira zinthu zopatulika kwambiri. Onani mutuwo |