Numeri 4:5 - Buku Lopatulika5 akati amuke a m'chigono, Aroni ndi ana ake aamuna azilowa, natsitse nsalu yotchinga, ndi kuphimba nayo likasa la mboni, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 akati amuke a m'chigono, Aroni ndi ana ake amuna azilowa, natsitse nsalu yotchinga, ndi kuphimba nayo likasa la mboni, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Pamene anthu akusamuka pamodzi ndi mahema ao, Aroni pamodzi ndi ana ake aloŵe m'chihema chamsonkhano, amasule nsalu yochinga, ndipo aphimbire Bokosi laumboni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Pamene anthu akusamuka pa msasa, Aaroni ndi ana ake aamuna azilowa mu tenti ndi kuchotsa chinsalu chotchingira ndi kuphimba nacho bokosi la umboni. Onani mutuwo |