Numeri 4:25 - Buku Lopatulika25 azinyamula nsalu zophimba za Kachisi, ndi chihema chokomanako, chophimba chake, ndi chophimba cha zikopa za akatumbu chili pamwamba pake, ndi nsalu yotsekera pa khomo la chihema chokomanako; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 azinyamula nsalu zophimba za Kachisi, ndi chihema chokomanako, chophimba chake, ndi chophimba cha zikopa za akatumbu chili pamwamba pake, ndi nsalu yotsekera pa khomo la chihema chokomanako; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 azinyamula nsalu zochinga malo opatulika, chihema chamsonkhano pamodzi ndi chophimbira chake, zikopa zambuzi zophimba pamwamba pake, ndiponso nsalu zochinga pa khomo la chihema chamsonkhano. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Azinyamula makatani a ku chihema, tenti ya msonkhano, zokutira zake ndi zokutira kunja za zikopa za akatumbu, makatani a pa khomo la ku tenti ya msonkhano, Onani mutuwo |