Numeri 4:24 - Buku Lopatulika24 Ntchito ya mabanja a Ageresoni, pogwira ntchito ndi kusenza katundu ndi iyi; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Ntchito ya mabanja a Ageresoni, pogwira ntchito ndi kusenza katundu ndi iyi; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Zimene mabanja a Geresoni ayenera kuchita, ndiponso zimene ayenera kumanyamula ndi izi: Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 “Ntchito ya mafuko a Ageresoni pamene akugwira ntchito ndi kunyamula katundu ndi iyi: Onani mutuwo |