Numeri 34:7 - Buku Lopatulika7 Malire anu a kumpoto ndiwo: kuyambira ku Nyanja Yaikulu mulinge kuphiri la Hori: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Malire anu a kumpoto ndiwo: kuyambira ku Nyanja Yaikulu mulinge kuphiri la Hori: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 “Malire anu akumpoto ndi aŵa, mulembe malire kuyambira ku Nyanja yaikulu mpaka ku phiri la Hori. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 “ ‘Malire anu a kumpoto, mzere wake uyambire ku Nyanja Yayikulu mpaka ku phiri la Hori Onani mutuwo |